Mphongo

CHORUS
Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)
VERSE ONE
Mkazi wanga ndi professional
Chikondi chake chiri sensational
Chikondi cha natural ma rehearsal no
Easy….musazitenge personal
Lol
Chikondi chake ndikuopa chindinenepetsa poti chachuluka starch
Kukhala naye sizitheka kungomuyang’ana I’m tempted to touch
Ndimadziwa amandikonda asananene akachita kuyankhula nde nanji
Chikondi chake ndi more..Yes I’m feeling all good

CHORUS
Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)

VERSE TWO
Mkazi wanga ali ndi vision
Chikondi chake cho no season
Amandikonda opanda reason
Kusokoneza please no
Ndimadziwa kusankha iye kuti akhale wa pa mtima sinnalakwitse yi
Zikanakhala zimatheka bwenzi ndikukhala naye like everyday
Okambawo amadziwa tilipobe no matter what they gonna say
We standing tall, lovings all the way
CHORUS
Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)

VERSE THREE
(DAN LU)
Babe mvera ndiwe number one
Pagulu la nzako umadya one
Ndikumva sugar
Ndikumva raga
It’s all good
(PIKSY – RAP)
Ndine mphongo yowilira
Musatsutse ndi mmene ndiku feelira
Ondifuna akuyenera kupilira
Ndikufewa mafana mwandilira
Vomerezani..mfana I’m rocking
Jus lay back man lemme do the talking
Yeah, ndikumva kukoma
Chofewa chimphongo chodziwika ndi boma
CHORUS
Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)

Ekleyen: nisanur cakmak
Bu şarkı sözü 29 kez okundu.